Levitiko 25:18 BL92

18 M'mwemo mucite malemba anga, ndi kusunga maweruzo anga, ndi kuwacita; ndipo mudzakhala m'dzikomo okhazikika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:18 nkhani