Levitiko 25:2 BL92

2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mutakalowa m'dziko limene ndikupatsani, dzikoli lizisungira Yehova Sabata.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:2 nkhani