Levitiko 25:42 BL92

42 Pakuti iwo ndiwo atumiki anga, amene ndinawaturutsa m'dziko la Aigupto; asamawagulitsa monga amagulitsa kapolo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:42 nkhani