Levitiko 25:47 BL92

47 Ndipo mlendo wakugonera kwanu akalemera cuma, ndi mbale wako wakukhala naye akasauka, nadzigulitsa kwa mlendo wakugonera kwanu, kapena kwa pfuko la banja la mlendo;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 25

Onani Levitiko 25:47 nkhani