5 Zophuka zokha zofikira masika usamazichera, ndi mphesa za mipesa yako yosadzombola usaziceka; cikhale caka copumula dziko.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 25
Onani Levitiko 25:5 nkhani