13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto, kuti musakhale akapolo ao; ndipo ndinatyola mitengo ya magoli anu, ndi kukuyendetsani coweramuka.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 26
Onani Levitiko 26:13 nkhani