15 ndipo mukakaniza malemba anga, ndi moyo wanu ukanyansidwa nao maweruzo anga, kotero kuti simudzacita malamulo anga onse, koma kutyola cipangano canga;
Werengani mutu wathunthu Levitiko 26
Onani Levitiko 26:15 nkhani