Levitiko 26:26 BL92

26 Pamene ndityola mcirikizo wanu wa mkate, akazi khumi adzaphika mkate wanu mu mcembo umodzi, nadzabweza mkate wanu ndi kuuyesa; ndipo mudzadya, koma osakhuta.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 26

Onani Levitiko 26:26 nkhani