28 Ine ndidzayenda nanu motsutsana mwa kukuzazirani, ndi kukulangani Inedi kasanu ndi kawiri cifukwa ca zocimwa zanu.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 26
Onani Levitiko 26:28 nkhani