Levitiko 27:15 BL92

15 Ndipo iye wakuipatula akaombola nyumba yace, aonjezepo limodzi la magawo asanu la ndalama za kuyesa kwako, ndipo idzakhala yace.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:15 nkhani