Levitiko 27:18 BL92

18 Akaupatula munda wace citapita caka coliza lipenga, wansembe azimwerengera ndalama monga mwa zaka zotsalira kufikira caka coliza lipenga, nazicepsako pa kuyesa kwako.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:18 nkhani