Levitiko 27:26 BL92

26 Komatu woyamba kubadwa mwa nyama akhale wobadwa woyamba wa Yehova, munthu asampatule; ingakhale ng'ombe ingakhale nkhosa, ndiye wa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 27

Onani Levitiko 27:26 nkhani