Levitiko 3:16 BL92

16 Ndipo wansembe atenthe izi pa guwa la nsembe; ndizo cakudya ca nsembe yamoto icite pfungo lokoma; mafuta onse nga Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 3

Onani Levitiko 3:16 nkhani