Levitiko 4:12 BL92

12 inde ng'ombe yonse, kunja kwa cigono, kumka nayo kumalo koyera, kumene atayako mapulusa, naitenthe pankhuni ndi moto; aitenthe potayira mapulusa.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:12 nkhani