Levitiko 4:15 BL92

15 Ndipo akuru a khamulo aike manja ao pamutu pa ng'ombeyo, pamaso pa Yehova; naiphe ng'ombeyo pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:15 nkhani