Levitiko 4:30 BL92

30 Ndipo wansembe atengeko mwazi ndi cala cace, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wace wonse patsinde pa guwa la nsembe.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:30 nkhani