Levitiko 4:32 BL92

32 Ndipo akadza nayo nkhosa, ndiyo copereka cace, ikhale nsembe yaucimo, azidza nayo yaikazi, yopanda cirema.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:32 nkhani