Levitiko 4:34 BL92

34 Ndipo wansembe atengeko mwazi wa nsembe yaucimo ndi cala cace, nauike pa nyanga za guwa la nsembe yopsereza, ndi kuthira mwazi wace wonse patsinde pa guwa la nsembe;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 4

Onani Levitiko 4:34 nkhani