Levitiko 5:9 BL92

9 nawazeko mwazi wa nsembe yaucimo pa mbali ya guwa la nsembe; ndi mwazi wotsalira aukamulire patsinde pa guwa la nsembe; ndiyo nsembe yaucimo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 5

Onani Levitiko 5:9 nkhani