Levitiko 7:24 BL92

24 Ndipo mafuta a iyo idafa yokha, ndi mafuta a iyo idajiwa ndi cirombo ayenera nchito iri yonse, koma musamadya awa konse konse.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:24 nkhani