Levitiko 7:30 BL92

30 adze nazo m'manja mwace nsembe zamoto za Yehova; adze nao mafuta pamodzi ndi nganga, kuti aweyule ngangayo ikhale nsembe yoweyula pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:30 nkhani