Levitiko 7:38 BL92

38 cimene Yehova analamulira Mose m'phiri la Sinai, tsikuli anauza ana a Israyeli abwere nazo zopereka zao kwa Yehova, m'cipululu ca Sinai.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 7

Onani Levitiko 7:38 nkhani