Levitiko 8:14 BL92

14 Ndipo anabwera nayo ng'ombe ya nsembe yaucimo; ndipo Aroni ndi ana ace amuna anaika manja ao pa mutu wa ng'ombe ya nsembe yaucimo.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:14 nkhani