33 Ndipo musaturuka pa khomo la cihema cokomanako masiku asanu ndi awiri, kufikira anakwanira masiku a kudzaza manja kwanu; pakuti adzaze manja anu masiku asanu ndi awiri.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 8
Onani Levitiko 8:33 nkhani