Levitiko 8:9 BL92

9 Naika nduwirayo pamutu pace; ndi panduwira, pamphumi pace anaika golidi waphanthiphanthi, ndiwo korona wopatulika; monga Yehova adauza Mose.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 8

Onani Levitiko 8:9 nkhani