Levitiko 9:22 BL92

22 Ndipo Aroni anakweza dzanja lace kulozera anthu, nawadalitsa; natsika kuja anapereka nsembe yaucimo, ndi nsembe yopsereza, ndi nsembe zoyamika.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 9

Onani Levitiko 9:22 nkhani