6 Ndipo Mose anati, Ici ndi cimene Yehova anakuuzani kuti mucicite; ndipo ulemerero wa Yehova udzaonekera kwa inu.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 9
Onani Levitiko 9:6 nkhani