Yoswa 1:6 BL92

6 Khala wamphamvu, nulimbike mtima, pakuti udzagawira anthu awa dzikoli likhale colowa cao, ndilo limene ndinalumbirira makolo ao kuwapatsa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 1

Onani Yoswa 1:6 nkhani