Yoswa 10:7 BL92

7 Pamenepo Yoswa anakwera kucokera ku Giligala, iye ndi anthu onse a nkhondo pamodzi naye, ndi ngwazi yose.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:7 nkhani