8 Ndipo Yehova ananena ndi Yoswa, Usawaope, pakuti ndawapereka m'dzanja lako; palibe mmodzi wa iwo adzaima pamaso pako.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 10
Onani Yoswa 10:8 nkhani