Yoswa 13:7 BL92

7 Ndipo tsopano uwagawire mapfuko asanu ndi anai, ndi pfuko la Manase logawika pakati, dziko ili likhale colowa cao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:7 nkhani