Yoswa 13:9 BL92

9 kuyambira pa Aroeri, wokhala m'mphepete mwa cigwa ca Arinoni, ndi mudzi uti pakati pa cigwa, ndi cidikha conse ca Medeba mpaka ku Diboni;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 13

Onani Yoswa 13:9 nkhani