Yoswa 15:16 BL92

16 Ndipo Kalebe anati, iye amene akantha Kiriyati-Seferi, naulanda, yemweyo ndidzampatsa Akisa mwana wanga akhale mkazi wace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:16 nkhani