Yoswa 15:19 BL92

19 Nati iye, Mundipatse dalitso; popeza mwandipatsa dziko la kumwela, ndipatseninso zitsime za madzi. Pamenepo anampatsa zitsime za kumtunda, ndi zitsime za kunsi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 15

Onani Yoswa 15:19 nkhani