12 ndi kucokera ku Saridi anazungulira kumka kum'mawa kumaturukira dzuwa, mpaka malire a Kisilotu-tabori; naturuka kumka ku Daberati, nakwera ku Yafia;
Werengani mutu wathunthu Yoswa 19
Onani Yoswa 19:12 nkhani