40 Yonseyi ndiyo midzi ya ana a Merari monga mwa mabanja ao, ndiwo otsala a mabanja a Alevi; ndipo gawo lao ndilo midzi khumi ndi iwiri.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 21
Onani Yoswa 21:40 nkhani