41 Midzi yonse ya Alevi, pakati pa colowa ca ana a Israyeli ndiyo midzi makumi anai kudza isanu ndi itatu, ndi mabusa ao.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 21
Onani Yoswa 21:41 nkhani