6 Koma mulimbike mtima kwambiri kusunga ndi kucita zonse zolembedwa m'buku la cilamulo ca Mose, osacipambukira kulamanja kapena kulamanzere;
Werengani mutu wathunthu Yoswa 23
Onani Yoswa 23:6 nkhani