14 Nati, lai, koma ndadza ine, kazembe wa ankhondo a Yehova. Pamenepo Yoswa anagwa nkhope yace pansi, napembedza, nati kwa iye, Anenanji Ambuyanga kwa mtumiki wace?
Werengani mutu wathunthu Yoswa 5
Onani Yoswa 5:14 nkhani