Yoswa 5:15 BL92

15 Ndipo kazembe wa ankhondo a Yehova anati kwa Yoswa, Bvula nsapato yako pa phazi lako; pakuti malo upondapo mpopatulika. Nacita Yoswa comweco.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:15 nkhani