20 Ndipo Akani anayankha Yoswa nati, Zoonadi, ndacimwira Yehova Mulungu wa Israyeli, ndacita zakuti zakuti;
Werengani mutu wathunthu Yoswa 7
Onani Yoswa 7:20 nkhani