19 Ndipo Yoswa anati kwa Akani, Mwana wanga, ucitiretu ulemu Yehova Mulungu wa Israyeli, numlemekeze iye; nundiuze tsopano, wacitanji? usandibisire.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 7
Onani Yoswa 7:19 nkhani