Yoswa 7:18 BL92

18 nayandikizitsa a m'nyumba yace mmodzi mmodzi; ndipo Akani, mwana wa Karimu, mwanu wa Zabidi, mwana wa Zera, wa pfuko la Yuda anagwidwa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 7

Onani Yoswa 7:18 nkhani