19 Nauka msanga olalirawo m'mbuto mwao, nathamanga pamene anatambasula dzanja lace, nalowa m'mudzi, naugwira; nafulumira nayatsa mudziwo.
Werengani mutu wathunthu Yoswa 8
Onani Yoswa 8:19 nkhani