15 Ndipo wansembe abwere naco ku guwa la nsembe, namwetule mutu wace, naitenthe pa guwa la nsembe; ndi mwazi wace aukamulire pa mbali ya guwa la nsembe,
Werengani mutu wathunthu Levitiko 1
Onani Levitiko 1:15 nkhani