Levitiko 1:14 BL92

14 Ndipo copereka cace ca kwa Yehova cikakhala nsembe yopsereza ya mbalame, azibwera naco copereka cace cikhale ca njiwa, kapena ca maunda.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:14 nkhani