Levitiko 1:13 BL92

13 Koma atsuke ndi madzi matumbo ndi miyendo; ndi wansembe abwere nazo zonse nazitenthe pa guwa la nsembe; ndiyo nsembe yopsereza, nsembe yamoto, ya pfungo lokoma la kwa Yehova.

Werengani mutu wathunthu Levitiko 1

Onani Levitiko 1:13 nkhani