12 Ndipo aikadzule ziwalo zace, pamodzi ndi mutu wace ndi mafuta ace; ndi wansembeyo akonze izi pa nkhuni ziri pa mota wa pa guwa la nsembe.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 1
Onani Levitiko 1:12 nkhani