20 ndipo taonani, ngati cioneka cakumba kubzola khungu, ndipo tsitsi lace lisanduka lotuwa, pamenepo wansembe amuche wodetsedwa; ndiyo nthenda yakhate yabuka m'cirondamo.
Werengani mutu wathunthu Levitiko 13
Onani Levitiko 13:20 nkhani