Levitiko 13:21 BL92

21 Koma wansembe akaciona, ndipo taonani, palibe tsitsi loyera pamenepo, ndipo sicinakumba kubzola khungu, koma cazimba, pamenepo wansembe ambindikiritse masiku asanu ndi awiri;

Werengani mutu wathunthu Levitiko 13

Onani Levitiko 13:21 nkhani